2 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”