2 Samueli 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo Husai, mnzake wa Davide,+ anabwerera kumzinda. Ndipo Abisalomu+ anabwera ku Yerusalemu. 1 Mbiri 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahitofeli+ anali phungu+ wa mfumu ndipo Husai+ Mwareki+ anali mnzake wa mfumu.+