1 Mbiri 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahitofeli+ anali mlangizi wa mfumu ndipo Husai+ mbadwa ya Areki anali mnzake wa mfumu. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:33 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 29