2 Samueli 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Abisalomu anauza Husai kuti: “Kodi kumeneku ndiko umati kusonyeza mnzako kukoma mtima kosatha? N’chifukwa chiyani sunapite ndi mnzako?”+
17 Pamenepo Abisalomu anauza Husai kuti: “Kodi kumeneku ndiko umati kusonyeza mnzako kukoma mtima kosatha? N’chifukwa chiyani sunapite ndi mnzako?”+