2 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!” 1 Mbiri 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahitofeli+ anali phungu+ wa mfumu ndipo Husai+ Mwareki+ anali mnzake wa mfumu.+ Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
17 Bwenzi lenileni limakukonda nthawi zonse,+ ndipo bwenzilo ndi m’bale amene anabadwira kuti akuthandize pakagwa mavuto.+