1 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati ndingachedwe, ndalemba izi kuti udziwe mmene uyenera kuchitira m’nyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza+ choonadi.
15 Koma ngati ndingachedwe, ndalemba izi kuti udziwe mmene uyenera kuchitira m’nyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza+ choonadi.