2 Mbiri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+
7 Kenako anapanga zoikapo nyale+ 10 zagolide zofanana,+ n’kuziika m’kachisi. Anaika zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere.+