2 Mbiri 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anapanganso matebulo 10 n’kuwaika m’kachisi. Anaika asanu mbali ya kudzanja lamanja, asanu mbali ya kumanzere,+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide. 2 Mbiri 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Solomo anapanga ziwiya zonse+ zimene zinali panyumba ya Mulungu woona, guwa lansembe lagolide,+ matebulo+ oikapo mkate wachionetsero,
8 Anapanganso matebulo 10 n’kuwaika m’kachisi. Anaika asanu mbali ya kudzanja lamanja, asanu mbali ya kumanzere,+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide.
19 Solomo anapanga ziwiya zonse+ zimene zinali panyumba ya Mulungu woona, guwa lansembe lagolide,+ matebulo+ oikapo mkate wachionetsero,