2 Mafumu 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga zopalira moto ndi mbale zolowa zomwe zinali zagolide weniweni,+ komanso zomwe zinali zasiliva weniweni.+
15 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga zopalira moto ndi mbale zolowa zomwe zinali zagolide weniweni,+ komanso zomwe zinali zasiliva weniweni.+