Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 mabeseni, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu,+ ndi zopalira moto.+ Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino. Anapanganso molowa miyendo ya zitseko+ za chipinda chamkati, kutanthauza Chipinda Choyera Koposa, ndiponso molowa miyendo ya zitseko+ za nyumbayo.+ Zonsezi zinali zagolide.

  • Ezara 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Panalinso mbale 30 zing’onozing’ono zolowa+ zagolide, mbale 410 zing’onozing’ono zolowa zasiliva zogwiritsira ntchito zina, ndi ziwiya zina 1,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena