2 Mafumu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma sanapange mabeseni asiliva, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ malipenga,+ ndi ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za m’nyumba ya Yehova kuchokera pa ndalama zimene anthu anali kubweretsa kunyumba ya Yehova,+ Yeremiya 52:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo,+ zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu ndi ziwiya zonse zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.+
13 Koma sanapange mabeseni asiliva, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ malipenga,+ ndi ziwiya zilizonse zagolide kapena zasiliva za m’nyumba ya Yehova kuchokera pa ndalama zimene anthu anali kubweretsa kunyumba ya Yehova,+
18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo,+ zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu ndi ziwiya zonse zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.+