9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ n’kupitirira mpaka kumizinda ya m’mphepete mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu.+
5 Chotero, Davide anasonkhanitsa+ Aisiraeli onse kuchokera kumtsinje wa Iguputo+ mpaka kukafika polowera ku Hamati,+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu.+