1 Samueli 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Davide anali atatenganso Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ ndipo onse awiriwa anakhala akazi ake.+