Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Davide anapitiriza kukhala ndi Akisi ku Gati. Iye anakhala kumeneko pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye, ndipo aliyense mwa amunawo anali ndi banja lake.+ Davide anali ndi akazi ake awiri aja, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.

  • 2 Samueli 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawiyi, Davide anabereka ana aamuna+ ku Heburoni,+ ndipo mwana wake woyamba anali Aminoni+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli.

  • 1 Mbiri 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana amene Davide+ anabereka ku Heburoni+ anali awa: woyamba Aminoni,+ wobadwa kwa Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ wachiwiri Danieli, wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena