Salimo 127:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.
5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.