1 Samueli 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akazi awiri a Davide nawonso anali atatengedwa, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala. 2 Samueli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. 2 Samueli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako+ ndi akazi a mbuye wako+ pachifuwa chako. Ndinakupatsanso nyumba ya Isiraeli ndi ya Yuda.+ Zinthu zimenezi zikanakhala kuti sizinakukwanire, ndinali wokonzeka kuziwonjezera ndiponso kukupatsa zinthu zina.+
5 Akazi awiri a Davide nawonso anali atatengedwa, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.
13 Pambuyo pake, Davide anatenganso adzakazi+ ndi akazi+ ena mu Yerusalemu atachoka ku Heburoni, moti anaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.
8 Ine ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako+ ndi akazi a mbuye wako+ pachifuwa chako. Ndinakupatsanso nyumba ya Isiraeli ndi ya Yuda.+ Zinthu zimenezi zikanakhala kuti sizinakukwanire, ndinali wokonzeka kuziwonjezera ndiponso kukupatsa zinthu zina.+