2 Samueli 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwangondiuza kumene kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka m’tsogolo kwambiri. Limenelitu ndi lamulo limene mwapereka kwa anthu,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+ Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+
19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwangondiuza kumene kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka m’tsogolo kwambiri. Limenelitu ndi lamulo limene mwapereka kwa anthu,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+
11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+
17 Mphatso iliyonse yabwino+ ndi yangwiro imachokera kumwamba,+ pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo,+ ndipo iye sasintha ngati kusuntha kwa mthunzi.+