1 Mbiri 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu,+ kuwonjezeranso pamenepa+ mwandiuza kuti nyumba ya ine mtumiki wanu idzakhazikika mpaka nthawi yam’tsogolo,+ ndipo inu Yehova Mulungu, mwanditenga ine ngati munthu woyenera kukwezedwa.+
17 Inu Mulungu,+ kuwonjezeranso pamenepa+ mwandiuza kuti nyumba ya ine mtumiki wanu idzakhazikika mpaka nthawi yam’tsogolo,+ ndipo inu Yehova Mulungu, mwanditenga ine ngati munthu woyenera kukwezedwa.+