Genesis 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ana a adzakazi amene Abulahamu anali nawo, anawapatsa mphatso.+ Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo+ Kum’mawa,+ kutali ndi mwana wake Isaki. 2 Samueli 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba. 1 Mbiri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa ndiwo anali ana onse a Davide, kuwonjezera pa ana a adzakazi ake, ndipo Tamara+ anali mlongo wawo.
6 Koma ana a adzakazi amene Abulahamu anali nawo, anawapatsa mphatso.+ Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo+ Kum’mawa,+ kutali ndi mwana wake Isaki.
16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba.
9 Amenewa ndiwo anali ana onse a Davide, kuwonjezera pa ana a adzakazi ake, ndipo Tamara+ anali mlongo wawo.