Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Yehova wanena kuti, ‘Taona, ndikukugwetsera tsoka m’nyumba yako yomwe.+ Ndidzatenga akazi ako iwe ukuona ndi kuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi ako anthu onse akuona.+

  • 2 Samueli 16:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.”

  • 2 Samueli 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Patapita nthawi, Davide anafika kunyumba yake ku Yerusalemu.+ Ndiyeno mfumuyo inatenga akazi 10+ aja, adzakazi amene anawasiya kuti azisamalira nyumba yake, ndipo anawatsekera m’nyumba ina koma anapitiriza kuwapatsa chakudya. Iye sanagone nawonso,+ koma anawatsekerabe kufikira tsiku la kufa kwawo. Iwo anakhala akazi amasiye mwamuna wawo ali moyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena