2 Samueli 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba. 2 Samueli 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.”
16 Choncho mfumu inanyamuka ndi kutuluka ndipo anthu onse a m’nyumba yake anaitsatira.+ Koma mfumuyo inasiya akazi 10, amene anali adzakazi ake,+ kuti asamalire nyumba.
21 Pamenepo Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Ugone ndi adzakazi a bambo ako+ amene wawasiya kuti azisamalira nyumba.+ Ukatero Aisiraeli onse adzamva kuti wadzinunkhitsa+ pamaso pa bambo ako,+ ndipo manja+ a anthu onse amene ali ndi iwe adzalimba ndithu.”