1 Samueli 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Davide anali atatenganso Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ ndipo onse awiriwa anakhala akazi ake.+ 2 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Davide anapita kumeneko pamodzi ndi akazi ake awiri, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.
2 Chotero Davide anapita kumeneko pamodzi ndi akazi ake awiri, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.