1 Samueli 25:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Davide anali atatenganso Ahinowamu+ wa ku Yezereeli,+ ndipo onse awiriwa anakhala akazi ake.+ 1 Samueli 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akazi awiri a Davide nawonso anali atatengedwa, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.
5 Akazi awiri a Davide nawonso anali atatengedwa, Ahinowamu+ wa ku Yezereeli ndi Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala.