2 Mbiri 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ahazi+ anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16.+ Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova monga anachitira Davide kholo lake.+ Mateyu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uziya anabereka Yotamu.+Yotamu anabereka Ahazi.+Ahazi anabereka Hezekiya.+
28 Ahazi+ anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16.+ Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova monga anachitira Davide kholo lake.+