1 Mafumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ukayenda m’njira zanga mwa kusunga malangizo ndi malamulo anga+ monga momwe Davide bambo ako anayendera,+ ndidzatalikitsanso masiku ako.”+
14 Ndipo ukayenda m’njira zanga mwa kusunga malangizo ndi malamulo anga+ monga momwe Davide bambo ako anayendera,+ ndidzatalikitsanso masiku ako.”+