1 Mafumu 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+ 2 Mbiri 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iweyo ukayenda pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, mwa kuchita zonse zimene ndakulamula+ ndi kusunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+
5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+
17 “Iweyo ukayenda pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, mwa kuchita zonse zimene ndakulamula+ ndi kusunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+