Deuteronomo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Salimo 91:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzamukhutiritsa ndi masiku ambiri,+Ndipo ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Miyambo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Masiku ochuluka ali m’dzanja lake lamanja.+ M’dzanja lake lamanzere muli chuma ndi ulemerero.+
15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+