2 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+ Mateyu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uziya anabereka Yotamu.+Yotamu anabereka Ahazi.+Ahazi anabereka Hezekiya.+
29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+