2 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’chaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu. Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+ Hoseya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula+ ndi Hoseya+ mwana wa Beeri m’masiku+ a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda, ndiponso m’masiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli. Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.
18 M’chaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu.
1 Masomphenya+ amene Yesaya+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu m’masiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
1 Yehova analankhula+ ndi Hoseya+ mwana wa Beeri m’masiku+ a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda, ndiponso m’masiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli.