2 Mafumu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu m’chaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi wathunthu.+ 2 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+
13 Salumu mwana wa Yabesi, anakhala mfumu m’chaka cha 39 cha Uziya+ mfumu ya Yuda. Iye analamulira ku Samariya kwa mwezi umodzi wathunthu.+
26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+