Yeremiya 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mahatchi pitani. Inu magaleta thamangani ndi liwiro lalikulu! Lolani amuna amphamvu kuti apite. Lolani Kusi+ ndi Puti+ amene amadziwa kugwiritsira ntchito chishango kuti apite. Lolaninso Aludi+ amene amadziwa kukunga ndi kuponya uta kuti apite. Nahumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mphamvu zake zonse zinali kuchokera ku Itiyopiya komanso ku Iguputo,+ ndipo zinali zopanda malire. Anthu a ku Puti komanso a ku Libiya anali kumuthandiza.+
9 Inu mahatchi pitani. Inu magaleta thamangani ndi liwiro lalikulu! Lolani amuna amphamvu kuti apite. Lolani Kusi+ ndi Puti+ amene amadziwa kugwiritsira ntchito chishango kuti apite. Lolaninso Aludi+ amene amadziwa kukunga ndi kuponya uta kuti apite.
9 Mphamvu zake zonse zinali kuchokera ku Itiyopiya komanso ku Iguputo,+ ndipo zinali zopanda malire. Anthu a ku Puti komanso a ku Libiya anali kumuthandiza.+