Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ana a Hamu anali Kusi,+ Miziraimu,+ Puti+ ndi Kanani.+

  • 2 Mbiri 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kodi Aitiyopiya+ ndi Alibiya+ sanali gulu lankhondo lalikulu, la anthu ambiri, magaleta ambiri, ndi okwera pamahatchi ambirinso?+ Chifukwa chakuti munadalira Yehova, kodi iye sanawapereke m’manja mwanu?+

  • Yeremiya 46:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Inu mahatchi pitani. Inu magaleta thamangani ndi liwiro lalikulu! Lolani amuna amphamvu kuti apite. Lolani Kusi+ ndi Puti+ amene amadziwa kugwiritsira ntchito chishango kuti apite. Lolaninso Aludi+ amene amadziwa kukunga ndi kuponya uta kuti apite.

  • Ezekieli 27:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amuna a ku Perisiya,+ ku Ludi+ ndi ku Puti+ anali m’gulu lako lankhondo, anali m’gulu la asilikali ako. Amuna amenewa anali kupachika zishango ndi zisoti mwa iwe.+ Iwo ndi amene anakuchititsa kukhala waulemerero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena