1 Mbiri 2:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Mabanja a alembi amene anali kukhala ku Yabezi+ anali Atirati, Asimeati, ndi Asukati. Amenewa anali Akeni+ amene anachokera kwa Hamati bambo wa nyumba ya Rekabu.+
55 Mabanja a alembi amene anali kukhala ku Yabezi+ anali Atirati, Asimeati, ndi Asukati. Amenewa anali Akeni+ amene anachokera kwa Hamati bambo wa nyumba ya Rekabu.+