1 Mbiri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yabezi+ anali wolemekezeka kwambiri+ kuposa abale ake, ndipo mayi ake ndiwo anamutcha Yabezi,* chifukwa anati: “Ndam’bereka ndikumva ululu.”+
9 Yabezi+ anali wolemekezeka kwambiri+ kuposa abale ake, ndipo mayi ake ndiwo anamutcha Yabezi,* chifukwa anati: “Ndam’bereka ndikumva ululu.”+