Genesis 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+
16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+