1 Mbiri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yabezi anali wolemekezeka kwambiri kuposa azichimwene ake ndipo mayi ake anamupatsa dzina lakuti Yabezi,* chifukwa anati: “Ndamʼbereka ndikumva ululu.” 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 23
9 Yabezi anali wolemekezeka kwambiri kuposa azichimwene ake ndipo mayi ake anamupatsa dzina lakuti Yabezi,* chifukwa anati: “Ndamʼbereka ndikumva ululu.”