2 Mafumu 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iweyo wamva zimene mafumu a Asuri anachita kumayiko onse amene anawawononga.+ Ndiye kodi iweyo ukuona ngati upulumuka?+ 2 Mbiri 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana a Amoni ndi ana a Mowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anawapha ndi kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+
11 Iweyo wamva zimene mafumu a Asuri anachita kumayiko onse amene anawawononga.+ Ndiye kodi iweyo ukuona ngati upulumuka?+
23 Ana a Amoni ndi ana a Mowabu anaukira anthu okhala kudera lamapiri la Seiri+ ndipo anawapha ndi kuwamaliza. Atatha kupha anthu a ku Seiri, iwo anaphana okhaokha.+