Genesis 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kusi anabereka Nimurodi,+ amene anali woyamba kukhala wamphamvu padziko lapansi. Mika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atsogoleriwo adzalanga dziko la Asuri ndi lupanga.+ Adzalanganso dziko la Nimurodi+ m’njira zake zonse zolowera m’dzikolo. Wolamulirayo adzatipulumutsa kwa Msuri.+ Adzatipulumutsa Msuriyo akadzangofika m’dziko lathu ndi kuponda nthaka yathu.
6 Atsogoleriwo adzalanga dziko la Asuri ndi lupanga.+ Adzalanganso dziko la Nimurodi+ m’njira zake zonse zolowera m’dzikolo. Wolamulirayo adzatipulumutsa kwa Msuri.+ Adzatipulumutsa Msuriyo akadzangofika m’dziko lathu ndi kuponda nthaka yathu.