Ekisodo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mwa ana a Merari, panali banja la Amali+ ndi banja la Amusi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Amerari.+ 1 Mbiri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Merari+ anali Mali ndi Musi.+ Ana a Mali anali Eleazara+ ndi Kisi.
19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+