Genesis 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nowa anakwanitsa zaka 500. Pambuyo pake iye anabereka Semu,+ Hamu+ ndi Yafeti.+