1 Samueli 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli. 1 Mbiri 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nera+ anabereka Kisi,+ Kisi anabereka Sauli,+ Sauli anabereka Yonatani,+ Malikisuwa,+ Abinadabu,+ ndi Esibaala.+
2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli.
39 Nera+ anabereka Kisi,+ Kisi anabereka Sauli,+ Sauli anabereka Yonatani,+ Malikisuwa,+ Abinadabu,+ ndi Esibaala.+