1 Mbiri 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maere a Supimu ndi a Hosa+ anagwera kumadzulo pafupi ndi Chipata cha Saleketi, pamsewu wopita kumtunda. Gulu limodzi la alonda+ linakhala moyandikana ndi gulu lina la alonda.+
16 Maere a Supimu ndi a Hosa+ anagwera kumadzulo pafupi ndi Chipata cha Saleketi, pamsewu wopita kumtunda. Gulu limodzi la alonda+ linakhala moyandikana ndi gulu lina la alonda.+