Ekisodo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Usaphe munthu.*+ 1 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+ Mateyu 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho iye anaponya ndalama zasiliva zija m’kachisi n’kuchoka, ndipo anakadzimangirira.+
13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+