1 Samueli 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anadula mutu wa Sauli+ ndi kumuvula zida zake. Kenako anatumiza uthenga+ m’dziko lonse la Afilisiti, kunyumba za mafano awo+ ndi kwa anthu awo.
9 Iwo anadula mutu wa Sauli+ ndi kumuvula zida zake. Kenako anatumiza uthenga+ m’dziko lonse la Afilisiti, kunyumba za mafano awo+ ndi kwa anthu awo.