2 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu inu musanene zimenezi mumzinda wa Gati.+Musalengeze zimenezi m’misewu ya Asikeloni,+Kuopera kuti ana aakazi a Afilisiti angasangalale,+Kuopera kuti ana aakazi a anthu osadulidwa angakondwere.
20 Anthu inu musanene zimenezi mumzinda wa Gati.+Musalengeze zimenezi m’misewu ya Asikeloni,+Kuopera kuti ana aakazi a Afilisiti angasangalale,+Kuopera kuti ana aakazi a anthu osadulidwa angakondwere.