Deuteronomo 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+ 1 Samueli 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anadula mutu wa Sauli+ ndi kumuvula zida zake. Kenako anatumiza uthenga+ m’dziko lonse la Afilisiti, kunyumba za mafano awo+ ndi kwa anthu awo.
27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+
9 Iwo anadula mutu wa Sauli+ ndi kumuvula zida zake. Kenako anatumiza uthenga+ m’dziko lonse la Afilisiti, kunyumba za mafano awo+ ndi kwa anthu awo.