Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 (Dera loyambira kukamtsinje kotuluka mu Nailo kum’mawa kwa Iguputo, kukafika kumpoto kumalire ndi Ekironi,+ ankalitcha dziko la Akanani.)+ Madera a Afilisitiwa akulamulidwa ndi olamulira ogwirizana asanu.+ Maderawo ndi Gaza,+ Asidodi,+ Asikeloni,+ Gati+ ndi Ekironi,+ komanso Aavi+ akukhala komweko.

  • Oweruza 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno olamulira ogwirizana a Afilisiti anasonkhana pamodzi kuti achite phwando lalikulu lopereka nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo, ndi kuchita chikondwerero, ndipo anali kunena kuti: “Mulungu wathu wapereka m’manja mwathu mdani wathu Samisoni!”+

  • 1 Samueli 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno zifanizo zagolide za matenda a mudzi zimene Afilisiti anapereka kwa Yehova monga nsembe ya kupalamula ndi izi:+ mzinda wa Asidodi+ unapereka chifanizo chimodzi, wa Gaza+ chimodzi, wa Asikeloni+ chimodzi, wa Gati+ chimodzi ndi wa Ekironi+ chimodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena