2 Samueli 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti ku Gobu, ndipo Elihanani+ mwana wa Yaare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliyati Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+
19 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti ku Gobu, ndipo Elihanani+ mwana wa Yaare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliyati Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+