1 Mbiri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani+ mwana wa Yairi anapha Lami m’bale wake wa Goliyati+ Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+
5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani+ mwana wa Yairi anapha Lami m’bale wake wa Goliyati+ Mgiti, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtanda wa owomba nsalu.+