Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi, dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali mikono 6 ndi chikhatho chimodzi.*+

  • 1 Samueli 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Wansembeyo poyankha anati: “Lupanga la Goliyati+ Mfilisiti amene unamukantha m’chigwa cha Ela+ lilipo. Lakulungidwa ndi nsalu ndipo lili kuseli kwa efodi.+ Ngati ungakonde kutenga limeneli, litenge, chifukwa palibenso lupanga lina.” Pamenepo Davide anati: “Palibe lina lingafanane nalo, ndipatseni limenelo.”

  • 1 Samueli 22:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo Ahimeleki anafunsira+ kwa Yehova m’malo mwa Davide, kenako anam’patsa chakudya+ ndi lupanga+ la Goliyati Mfilisiti.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena